1 Samueli 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ankachita zimenezi chaka chilichonse Hana akapita kunyumba ya Yehova.+ Penina ankamuzunza kwambiri moti Hana ankalira ndipo sankadya. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 15
7 Ankachita zimenezi chaka chilichonse Hana akapita kunyumba ya Yehova.+ Penina ankamuzunza kwambiri moti Hana ankalira ndipo sankadya.