1 Samueli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amadzutsa wonyozeka kumuchotsa pafumbi,Amachotsa osauka paphulusa,*+Kuti akhale ndi ana a mafumu,Ndipo amawapatsa mpando wolemekezeka. Chifukwa zolimbitsira dziko lapansi ndi za Yehova,+Ndipo anakhazika dziko lapansi pa zolimbitsirazo.
8 Amadzutsa wonyozeka kumuchotsa pafumbi,Amachotsa osauka paphulusa,*+Kuti akhale ndi ana a mafumu,Ndipo amawapatsa mpando wolemekezeka. Chifukwa zolimbitsira dziko lapansi ndi za Yehova,+Ndipo anakhazika dziko lapansi pa zolimbitsirazo.