-
1 Samueli 2:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Akatero ankapisa folokoyo mʼbeseni, mʼpoto wa zogwirira ziwiri, mumphika kapena mʼpoto wa chogwirira chimodzi. Ndiyeno wansembe ankatenga chilichonse chimene folokoyo yatulutsa. Zimenezi ndi zimene ankachitira Aisiraeli onse opita ku Silo.
-