1 Samueli 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno aliyense wotsala mʼnyumba yako adzafika nʼkumugwadira kuti amulipire ndalama ndi chakudya, ndipo adzati: “Ndiloleni chonde ndikhale wansembe kuti ndizipezako kachakudya.”’”+
36 Ndiyeno aliyense wotsala mʼnyumba yako adzafika nʼkumugwadira kuti amulipire ndalama ndi chakudya, ndipo adzati: “Ndiloleni chonde ndikhale wansembe kuti ndizipezako kachakudya.”’”+