1 Samueli 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyale ya Mulungu+ inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona mʼkachisi*+ wa Yehova mmene munali Likasa la Mulungu. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, ptsa. 21-22
3 Nyale ya Mulungu+ inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona mʼkachisi*+ wa Yehova mmene munali Likasa la Mulungu.