-
1 Samueli 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho anathamangira kwa Eli nʼkunena kuti: “Ndabwera mbuyanga, ndamva kuitana.” Koma Eli anamuuza kuti: “Sindinakuitane. Pita ukagone.” Atatero Samueli anapita kukagonanso.
-