-
1 Samueli 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Yehova anaitananso kachitatu kuti: “Samueli!” Choncho Samueli anadzuka nʼkupita kwa Eli, ndipo ananena kuti: “Ndabwera, chifukwa mwandiitana ndithu.”
Zitatero Eli anazindikira kuti Yehova ndi amene ankaitana mwanayo.
-