-
1 Samueli 4:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Samueli analankhula ndi Aisiraeli onse.
Kenako Aisiraeli anapita kukamenyana ndi Afilisiti ndipo anamanga msasa pafupi ndi Ebenezeri. Koma Afilisiti anamanga msasa ku Afeki.
-