-
1 Samueli 4:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Afilisiti atamva phokosolo anafunsa kuti: “Kodi phokosoli, lomwe likumveka mumsasa wa Aheberi ndi la chiyani?” Kenako anamva kuti Likasa la Yehova labwera mumsasawo.
-