-
1 Samueli 4:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Munthu uja anauza Eli kuti: “Ine ndikuchokera kunkhondo ndipo ndachokako chothawa lero lomwe.” Choncho Eli anamufunsa kuti: “Kwachitika zotani mwana wanga?”
-