-
1 Samueli 4:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mpongozi wake, mkazi wa Pinihasi, anali woyembekezera ndipo anali pafupi kubereka. Atamva kuti Likasa la Mulungu woona lalandidwa komanso apongozi ake ndi mwamuna wake afa, matenda anamuyamba mwadzidzidzi ndipo anabereka mwana.
-