-
1 Samueli 4:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mkaziyu atatsala pangʼono kumwalira, amayi amene anaima pambali pake anamuuza kuti: “Usaope, wabereka mwana wamwamuna.” Koma iye sanayankhe komanso sanachite chilichonse.
-