-
1 Samueli 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Nʼchifukwa chake ansembe a Dagoni ndi anthu onse omwe amalowa mʼnyumba ya Dagoni ku Asidodi saponda pakhomo la nyumba ya Dagoni mpaka lero.
-