1 Samueli 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Afilisiti anaitana ansembe ndi olosera+ nʼkuwafunsa kuti: “Kodi Likasa la Yehova titani nalo? Tiuzeni zimene tingachite polibweza kwawo.”
2 Ndiyeno Afilisiti anaitana ansembe ndi olosera+ nʼkuwafunsa kuti: “Kodi Likasa la Yehova titani nalo? Tiuzeni zimene tingachite polibweza kwawo.”