3 Iwo anayankha kuti: “Ngati mukubweza likasa lapangano la Yehova Mulungu wa Isiraeli, musalibweze popanda kupereka nsembe. Mulimonse mmene zingakhalire, muyenera kupereka nsembe yakupalamula.+ Mukatero mudzachira ndipo mudzadziwa chifukwa chake dzanja lake silinasiye kukukhaulitsani.”