1 Samueli 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukatero, mutenge Likasa la Yehova nʼkuliika mungoloyo. Ndiyeno mutenge zinthu zagolide zimene mukuzitumiza ngati nsembe yakupalamula nʼkuizika mʼbokosi lina pambali pa Likasalo,+ kenako mulitumize lizipita.
8 Mukatero, mutenge Likasa la Yehova nʼkuliika mungoloyo. Ndiyeno mutenge zinthu zagolide zimene mukuzitumiza ngati nsembe yakupalamula nʼkuizika mʼbokosi lina pambali pa Likasalo,+ kenako mulitumize lizipita.