-
1 Samueli 6:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Anthuwo anachitadi zimenezo. Anatenga ngʼombe ziwiri zimene zinali ndi ana nʼkuzimangirira kungolo, ndipo ana a ngʼombezo anawatsekera mʼkhola kunyumba.
-