-
1 Samueli 6:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiyeno anaika Likasa la Yehova mungoloyo. Anaikamonso bokosi lokhala ndi mbewa zagolide komanso zifaniziro za matenda awo a mudzi.
-