1 Samueli 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngʼombezo zinayamba kuyenda mumsewu wopita ku Beti-semesi.+ Zinkangoyenda mumsewu waukulu zikulira ndipo sizinakhotere kumanja kapena kumanzere. Apa nʼkuti olamulira a Afilisiti akuzitsatira pambuyo mpaka kukafika mʼmalire a Beti-semesi.
12 Ngʼombezo zinayamba kuyenda mumsewu wopita ku Beti-semesi.+ Zinkangoyenda mumsewu waukulu zikulira ndipo sizinakhotere kumanja kapena kumanzere. Apa nʼkuti olamulira a Afilisiti akuzitsatira pambuyo mpaka kukafika mʼmalire a Beti-semesi.