-
1 Samueli 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Anthu a ku Beti-semesi ankakolola tirigu mʼchigwa. Atakweza maso nʼkuona Likasa, anasangalala kwambiri.