1 Samueli 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Alevi+ anatsitsa Likasa la Yehova komanso bokosi mmene munali zinthu zagolide zija, nʼkuziika pamwala waukulu uja. Kenako amuna a ku Beti-semesi+ anapereka nsembe zopsereza komanso nsembe zina kwa Yehova tsiku limenelo.
15 Alevi+ anatsitsa Likasa la Yehova komanso bokosi mmene munali zinthu zagolide zija, nʼkuziika pamwala waukulu uja. Kenako amuna a ku Beti-semesi+ anapereka nsembe zopsereza komanso nsembe zina kwa Yehova tsiku limenelo.