-
1 Samueli 6:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Chiwerengero cha mbewa zagolide chinali chofanana ndi cha mizinda yonse ya Afilisiti yolamuliridwa ndi ndi olamulira 5 aja, kuyambira mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri mpaka kumidzi yopanda mipanda.
Mwala waukulu umene anaikapo Likasa la Yehova uli ngati mboni mpaka lero mʼmunda wa Yoswa, wa ku Beti-semesi.
-