1 Samueli 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anatumiza uthenga kwa anthu a ku Kiriyati-yearimu+ wakuti: “Afilisiti abweza Likasa la Yehova, bwerani mudzalitenge.”+
21 Kenako anatumiza uthenga kwa anthu a ku Kiriyati-yearimu+ wakuti: “Afilisiti abweza Likasa la Yehova, bwerani mudzalitenge.”+