1 Samueli 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Afilisiti atamva kuti Aisiraeli asonkhana ku Mizipa, olamulira awo+ ananyamuka kuti akamenyane ndi Aisiraeli. Ndipo Aisiraeli atamva zimenezi, anachita mantha chifukwa cha Afilisitiwo.
7 Afilisiti atamva kuti Aisiraeli asonkhana ku Mizipa, olamulira awo+ ananyamuka kuti akamenyane ndi Aisiraeli. Ndipo Aisiraeli atamva zimenezi, anachita mantha chifukwa cha Afilisitiwo.