1 Samueli 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Samueli anatenga mwala+ nʼkuuimika pakati pa Mizipa ndi Yesana ndipo anaupatsa dzina lakuti Ebenezeri,* popeza anati: “Mpaka pano Yehova akutithandizabe.”+
12 Kenako Samueli anatenga mwala+ nʼkuuimika pakati pa Mizipa ndi Yesana ndipo anaupatsa dzina lakuti Ebenezeri,* popeza anati: “Mpaka pano Yehova akutithandizabe.”+