1 Samueli 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana akewa sanatsatire chitsanzo chake. Iwo ankakonda kupeza phindu mwachinyengo,+ kulandira ziphuphu+ ndiponso kupotoza chilungamo.+
3 Ana akewa sanatsatire chitsanzo chake. Iwo ankakonda kupeza phindu mwachinyengo,+ kulandira ziphuphu+ ndiponso kupotoza chilungamo.+