1 Samueli 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana anu aakazi adzawatenga kuti azikapanga mafuta onunkhira komanso azikaphika mikate ndi zakudya zina.+
13 Ana anu aakazi adzawatenga kuti azikapanga mafuta onunkhira komanso azikaphika mikate ndi zakudya zina.+