1 Samueli 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova anauza Samueli kuti: “Mvera zimene anenazo ndipo asankhire mfumu yoti iziwalamulira.”+ Kenako Samueli anauza Aisiraeliwo kuti: “Aliyense apite kumzinda wakwawo.”
22 Yehova anauza Samueli kuti: “Mvera zimene anenazo ndipo asankhire mfumu yoti iziwalamulira.”+ Kenako Samueli anauza Aisiraeliwo kuti: “Aliyense apite kumzinda wakwawo.”