1 Samueli 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika mʼdera la Zufi, Sauli anauza wantchito wake uja kuti: “Tiye tibwerere kunyumba, chifukwa bambo anga angasiye kuganizira za abulu nʼkuyamba kutidera nkhawa ifeyo.”+
5 Atafika mʼdera la Zufi, Sauli anauza wantchito wake uja kuti: “Tiye tibwerere kunyumba, chifukwa bambo anga angasiye kuganizira za abulu nʼkuyamba kutidera nkhawa ifeyo.”+