1 Samueli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wantchitoyo anauza Sauli kuti: “Ndili ndi siliva* woti ndingakapatse munthu wa Mulungu woonayo ndipo akatiuza kumene tingalowere.”
8 Wantchitoyo anauza Sauli kuti: “Ndili ndi siliva* woti ndingakapatse munthu wa Mulungu woonayo ndipo akatiuza kumene tingalowere.”