-
1 Samueli 9:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako Sauli anauza wantchito wakeyo kuti: “Maganizo abwino. Tiye tipite.” Choncho anapita kumzinda kumene kunali munthu wa Mulungu woonayo.
-