1 Samueli 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene ankakwera mtunda kuti akalowe mumzindawo, anakumana ndi atsikana akupita kukatunga madzi, ndipo anawafunsa kuti: “Kodi wamasomphenya+ ali mumzindawu?”
11 Pamene ankakwera mtunda kuti akalowe mumzindawo, anakumana ndi atsikana akupita kukatunga madzi, ndipo anawafunsa kuti: “Kodi wamasomphenya+ ali mumzindawu?”