-
1 Samueli 9:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Choncho anapita kukalowa mumzindawo. Atatsala pangʼono kufika pakati pa mzindawo, anangoona Samueli akubwera kudzakumana nawo kuti apite kumalo okwezeka.
-