1 Samueli 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma musadandaule za abulu amene anasowa masiku atatu apitawo+ chifukwa anapezeka. Ndipo kodi zabwino zonse mu Isiraeli ndi za ndani? Mmesa ndi zako ndi anthu onse amʼnyumba ya bambo ako?”+
20 Koma musadandaule za abulu amene anasowa masiku atatu apitawo+ chifukwa anapezeka. Ndipo kodi zabwino zonse mu Isiraeli ndi za ndani? Mmesa ndi zako ndi anthu onse amʼnyumba ya bambo ako?”+