-
1 Samueli 9:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndiyeno Samueli anatenga Sauli ndi wantchito wake nʼkupita nawo mʼchipinda chodyera. Atafika, anawapatsa malo apamwamba kuposa oitanidwa ena onse. Mʼchipindamo munali anthu pafupifupi 30.
-