1 Samueli 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero, anatsika pamalo okwezeka+ aja nʼkupita mumzinda ndipo Samueli anapitiriza kulankhula ndi Sauli ali padenga la nyumba. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:25 Nsanja ya Olonda,4/15/2015, tsa. 6
25 Zitatero, anatsika pamalo okwezeka+ aja nʼkupita mumzinda ndipo Samueli anapitiriza kulankhula ndi Sauli ali padenga la nyumba.