1 Samueli 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene ankayandikira chakumapeto kwa mzindawo, Samueli anauza Sauli kuti: “Muuze wantchito wakoyu+ atsogole, koma iweyo uime kaye kuti ndikuuze mawu a Mulungu.” Atatero, wantchitoyo anatsogola.
27 Pamene ankayandikira chakumapeto kwa mzindawo, Samueli anauza Sauli kuti: “Muuze wantchito wakoyu+ atsogole, koma iweyo uime kaye kuti ndikuuze mawu a Mulungu.” Atatero, wantchitoyo anatsogola.