-
1 Samueli 11:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Nahasi Muamoni ananena kuti: “Ndichita nanu pangano pokhapokha ngati aliyense wa inu nditamuboola diso lake lakumanja. Ndichita zimenezi kuti ndichititse manyazi Aisiraeli onse.”
-