-
1 Samueli 11:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Akulu a ku Yabesi anayankha kuti: “Mutipatse masiku 7 kuti titumize uthenga mʼdziko lonse la Isiraeli, ngati sipapezeka wotipulumutsa, tidzadzipereka kwa inu.”
-