-
1 Samueli 11:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iye anatenga ngʼombe ziwiri zamphongo nʼkuzidula mapisi. Kenako anatuma anthu kuti akapereke mapisiwo mʼmadera onse a Isiraeli ndipo anati: “Aliyense amene satsatira Sauli ndi Samueli, izi nʼzimene zichitikire ngʼombe zake.” Anthu anagwidwa ndi mantha ochokera kwa Yehova, moti onse anapita mogwirizana.*
-