1 Samueli 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako iwo anauza anthu amene anabwera ndi uthenga aja kuti: “Anthu a ku Yabesi ku Giliyadi mukawauze kuti, ‘Mawa masana* mupulumutsidwa.’” Zitatero anthuwo anafika ku Yabesi nʼkuuza anthu akumeneko uthengawo ndipo iwo anasangalala kwambiri.
9 Kenako iwo anauza anthu amene anabwera ndi uthenga aja kuti: “Anthu a ku Yabesi ku Giliyadi mukawauze kuti, ‘Mawa masana* mupulumutsidwa.’” Zitatero anthuwo anafika ku Yabesi nʼkuuza anthu akumeneko uthengawo ndipo iwo anasangalala kwambiri.