1 Samueli 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pomaliza, Samueli anauza Aisiraeli onse kuti: “Ndachita zonse zimene* munandiuza, ndipo ndakusankhirani mfumu yoti izikulamulirani.+
12 Pomaliza, Samueli anauza Aisiraeli onse kuti: “Ndachita zonse zimene* munandiuza, ndipo ndakusankhirani mfumu yoti izikulamulirani.+