1 Samueli 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atatero, iye anawayankha kuti: “Yehova ndi mboni yokutsutsani ndipo nayenso wodzozedwa wake ndi mboni lero kuti simunandipeze ndi mlandu uliwonse.”* Iwo anati: “Inde, iye ndi mboni.”
5 Atatero, iye anawayankha kuti: “Yehova ndi mboni yokutsutsani ndipo nayenso wodzozedwa wake ndi mboni lero kuti simunandipeze ndi mlandu uliwonse.”* Iwo anati: “Inde, iye ndi mboni.”