1 Samueli 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi ino si nthawi yokolola tirigu? Ndipemphera kwa Yehova kuti abweretse mabingu ndi mvula. Zikatero mudziwa ndiponso kuzindikira kuti mwachita zoipa kwambiri pamaso pa Yehova popempha kuti mukhale ndi mfumu.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:17 Tsanzirani, tsa. 59 Nsanja ya Olonda,10/1/2010, tsa. 14
17 Kodi ino si nthawi yokolola tirigu? Ndipemphera kwa Yehova kuti abweretse mabingu ndi mvula. Zikatero mudziwa ndiponso kuzindikira kuti mwachita zoipa kwambiri pamaso pa Yehova popempha kuti mukhale ndi mfumu.”+