1 Samueli 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Sauli anali ndi zaka . . .* pamene anakhala mfumu,+ ndipo analamulira Isiraeli zaka ziwiri.