1 Samueli 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yonatani anapha asilikali a Afilisiti+ amene anali ku Geba+ ndipo Afilisiti anamva zimenezi. Zitatero Sauli analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ mʼdziko lonse nʼkunena kuti: “Tamverani Aheberi nonse!”
3 Kenako Yonatani anapha asilikali a Afilisiti+ amene anali ku Geba+ ndipo Afilisiti anamva zimenezi. Zitatero Sauli analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ mʼdziko lonse nʼkunena kuti: “Tamverani Aheberi nonse!”