1 Samueli 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aisiraeli onse anamva nkhani yakuti: “Sauli wapha asilikali a Afilisiti moti panopa Aisiraeli akhala chinthu chonunkha kwa Afilisiti.” Choncho anasonkhanitsa anthu onse kuti atsatire Sauli ku Giligala.+
4 Aisiraeli onse anamva nkhani yakuti: “Sauli wapha asilikali a Afilisiti moti panopa Aisiraeli akhala chinthu chonunkha kwa Afilisiti.” Choncho anasonkhanitsa anthu onse kuti atsatire Sauli ku Giligala.+