-
1 Samueli 13:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiye ndinaganiza kuti, ‘Afilisitiwa abwera ku Giligala kuno kudzamenyana nane, ndipo sindinakhazike pansi mtima wa Yehova.’ Choncho ndinaona kuti ndiyenera kupereka nsembe yopsereza.”
-