1 Samueli 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Gulu lachiwiri linkalowera kumsewu wa ku Beti-horoni,+ ndipo gulu lachitatu linkalowera kumsewu wopita kumalire oyangʼanizana ndi chigwa cha Zeboyimu, molunjika kuchipululu.
18 Gulu lachiwiri linkalowera kumsewu wa ku Beti-horoni,+ ndipo gulu lachitatu linkalowera kumsewu wopita kumalire oyangʼanizana ndi chigwa cha Zeboyimu, molunjika kuchipululu.