-
1 Samueli 13:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho Aisiraeli onse akafuna kunola pulawo, khasu, nkhwangwa kapena chikwakwa, ankapita kwa Afilisiti kuti akawanolere.
-